DESPERATE
Written by : Faith Mussa
Composed by: Faith Mussa
Guitar by Faith Mussa
Key of D#. Cappo placed on 3rd fret
Intro
Ine ndili desperate for your Love
Ine ndili desperate for your hand
Ine ndili desperate for your touch
Ine ndili desperate, deperate for You
Verse 1
Chilichonse chomwe ndili nacho chachokera kwa inu
Ngakhale ntchito yomwe tikugwirayi timayamika inu
Sukulu yonse yomwe taphunzirayi timayamika inu
Ngakhale magitala tikuimbawa timayamika inu
Ine ndili desperate for your Love
Ine ndili desperate for your hand
Ine ndili desperate for your touch
Ine ndili desperate, x2
Chorus
Ine ndili desperate
Ndili desperate
Ine ndili desperate
Ndili desperate
Ine ndili desperate, ndili desperate, ndili desperate,
Ine ndili desperate, ndili desperate, ndili desperate,
Verse2
Chilichonse chomwe ndidzachite ndidzatumikira inu
Ngakhale nyimbo zomwe ndidzaimbe, ndidzaimbira inu
Mtim wanga thupi langa zones, zidzatumikira inu
Ndikufuna mbuye mukamandiona, mudzingomwetulira
Ine ndili desperate for your Love
Ine ndili desperate for your hand
Ine ndili desperate for your touch
Ine ndili desperate, x2
Chorus
Ine ndili desperate
Ndili desperate
Ine ndili desperate
Ndili desperate
Ine ndili desperate, ndili desperate, ndili desperate,
Ine ndili desperate, ndili desperate, ndili desperate,
Bridge
Nthawi zonse ndimafuna,
Kuyenda nanu
Chikondi chanu chinazula
Mtima wanga
Mukandiona ndikukwera phiri, kukapemphera, ndili desperate
Ngakhale ndimayenda
Mnthunzi wa imfa
Sindidzaopa poti mbuye, Mulinane
Chibonga chanu nândodo yanu zindisangalatsa,
Ine ndili desperate for your Love
Ine ndili desperate for your hand
Ine ndili desperate for your touch
Ine ndili desperate, desperate for you!
For you, for you
Ndili desperate for you
For you, for you
Ine ndili desperate for you
For you, for you
ending
Ndikufuna Nkhope yanu Mbuye,
Ndikufuna nkono chanu Mbuye
Ndikufuna dzanja lanu mbuye, Edipo ndili desperate,
Ndikufuna zozizwa zanu mbuye,
Ndikufuna chiyero chanu mbuye
Ndikufuna dzanja lanu mbuye, Edipo ndili desperate,
Desperate for you